1 Yang'anirani kuti musacite zolungama zanu pamaso pa anthu kuti muonekere kwa iwo; pakuti ngati mutero mulibe mphotho ndi Atate wanu wa Kumwamba.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 6
Onani Mateyu 6:1 nkhani