15 Koma ngati simukhululukira anthu zolakwa zao, Atate wanunso sadzakhululukira zolakwa zanu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 6
Onani Mateyu 6:15 nkhani