Mateyu 6:19 BL92

19 Musadzikundikire nokha cuma pa dziko lapansi, pamene njenjete ndi dzimbiri ziononga; ndi pamene mbala ziboola ndi kuba:

Werengani mutu wathunthu Mateyu 6

Onani Mateyu 6:19 nkhani