Mateyu 6:32 BL92

32 Pakuti anthu akunja azifunitsa zonse zimenezo; pakuti Atate wanu wa Kumwamba adziwa kuti musowa zonse zimenezo.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 6

Onani Mateyu 6:32 nkhani