7 Ndipo popemphera musabwereze-bwereze cabe iai, monga amacita anthu akunja, cifukwa ayesa kuti adzamvedwa ndi kulankhula-lankhula kwao.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 6
Onani Mateyu 6:7 nkhani