21 Si yense wakunena kwa Ine, Ambuye, Ambuye, adzalowa mu Ufumu wa Kumwamba; koma wakucitayo cifuniro ca Atate wanga wa Kumwamba.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 7
Onani Mateyu 7:21 nkhani