Mateyu 7:23 BL92

23 Ndipo pamenepo ndidzafukulira iwo, Sindinakudziwani inu nthawi zonse; cokani kwa Ine, inu akucita kusayeruzika.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 7

Onani Mateyu 7:23 nkhani