Mateyu 7:25 BL92

25 ndipo inagwa mvula, nidzala mitsinje, ndipo zinaomba mphepo, zinagunda pa nyumbayo; koma siinagwa; cifukwa inakhazikika pathanthwepo.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 7

Onani Mateyu 7:25 nkhani