4 Kapena udzati bwanji kwa mbale wako, Tandilola ndicotse kacitsotso m'diso lako; ndipo ona, mtandawo ulimo m'diso lakoli.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 7
Onani Mateyu 7:4 nkhani