6 Musamapatsa copatulikaco kwa agaru, ndipo musamaponya ngale zanu patsogolo pa nkhumba, kuti zingazipondereze ndi mapazi ao, ndi potembenuka zingang'ambe inu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 7
Onani Mateyu 7:6 nkhani