Mateyu 8:10 BL92

10 Ndipo pakumva ici, Yesu anazizwa, nati kwa iwo akumtsata, Indetu ndinena kwa inu, ngakhale mwa Israyeli, sindinapeza cikhulupiriro cotere.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 8

Onani Mateyu 8:10 nkhani