20 Ndipo Yesu ananena kwa iye, Ankhandwe ali nazo nkhwimba zao, ndi mbalame za m'mlengalenga zisa zao, koma Mwana wa munthu alibe potsamira mutu wace.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 8
Onani Mateyu 8:20 nkhani