34 Ndipo onani, mudzi wonse unaturukira kukakumana naye Yesu, ndipo m'mene anamuona Iye, anampempha kuti acoke m'malire ao.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 8
Onani Mateyu 8:34 nkhani