Mateyu 8:4 BL92

4 Ndipo Yesu ananena naye, Ona, iwe, usauze munthu; koma muka, udzionetse wekha kwa wansembe, nupereke mtulo umene anaulamulira Mose, ukhale mboni kwaiwo.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 8

Onani Mateyu 8:4 nkhani