14 Pomwepo anadza kwa Iye ophunzira ace a Yohane, nati, Cifukwa ninji ife ndi Afarisi tisala kudya kawiri kawiri, koma ophunzira anu sasala?
Werengani mutu wathunthu Mateyu 9
Onani Mateyu 9:14 nkhani