22 Koma Yesu potembenuka ndi kuona iye anati, Limba mtima, mwana wamkaziwe, cikhulupiriro cako cakuciritsa. Ndipo mkaziyo anacira kuyambira nthawi yomweyo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 9
Onani Mateyu 9:22 nkhani