27 Ndipo popita Yesu kucokera kumeneko, anamtsata Iye anthu awiri akhungu, opfuula ndi kuti, Muticitire ife cifundo, mwana wa Davide.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 9
Onani Mateyu 9:27 nkhani