11 Nawakantha Yehu otsala onse a nyumba ya Ahabu m'Yezreeli, ndi omveka ace onse, ndi odziwana naye, ndi ansembe ace, mpaka sanatsala wa iye ndi mmodzi yense.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10
Onani 2 Mafumu 10:11 nkhani