2 Mafumu 10:18 BL92

18 Ndipo Yehu anasonkhanitsa anthu onse pamodzi, nanena nao, Ahabu anatumikira Baala pang'ono, koma Yehu adzamtumikira kwambiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:18 nkhani