2 Mafumu 10:2 BL92

2 Tsono akakufikani inu kalata uyu, popeza muli nao ana a mbuye wanu; muli naonso magareta ndi akavalo, ndi mudzi walinga, ndi zida,

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:2 nkhani