2 Mafumu 10:23 BL92

23 Nalowa Yehu ndi Yehonadabu mwana wa Rekabu m'nyumba ya Baala, nati kwa otumikira Baala, Mufunefune, nimuone asakhale nanu muno otumikira Yehova, koma otumikira Baala okha.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:23 nkhani