2 Mafumu 11:4 BL92

4 Koma caka cacisanu ndi ciwiri Yehoyada anaitanitsa atsogoleri a mazana a opha anthu, ndi a otumikira, nabwera nao kwa iye ku nyumba ya Yehova, napangana nao, nawalumbiritsa m'nyumba ya Yehova, nawaonetsa mwana wa mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 11

Onani 2 Mafumu 11:4 nkhani