2 Mafumu 11:6 BL92

6 ndi lina lizikhala ku cipata ca Suri, ndi lina ku cipata kumbuyo kwa otumikira; momwemo muzisunga nyumba, ndi kuicinjiriza.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 11

Onani 2 Mafumu 11:6 nkhani