11 Napereka ndarama zoyesedwa m'manja mwa iwo akucita nchitoyi, akuyang'anira nyumba ya Yehova; ndipo iwo analipira nazo amisiri a mitengo ndi omanga, akugwira nchito ya pa nyumba ya Yehova,
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 12
Onani 2 Mafumu 12:11 nkhani