2 Mafumu 12:17 BL92

17 Pamenepo Hazaeli mfumu ya Aramu anakwera, nathira nkhondo pa Gati, naulanda, nalunjikitsa nkhope yace kukwera ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 12

Onani 2 Mafumu 12:17 nkhani