2 Mafumu 12:19 BL92

19 Macitidwe ena tsono a Yoasi ndi zonse adazicita sizilembedwa kodi m'buku la macitidwe a mafumu a Yuda?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 12

Onani 2 Mafumu 12:19 nkhani