2 Mafumu 12:4 BL92

4 Ndipo Yoasi anati kwa ansembe, Landirani ndarama zonse za zinthu zopatulika azibwera nazo ku nyumba ya Yehova, ndizo ndarama za otha msinkhu, ndarama za munthu ali yense monga adamuyesa, ndi ndalama zimene yense azikumbuka m'mtima mwace kuti abwere nazo ku nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 12

Onani 2 Mafumu 12:4 nkhani