2 Mafumu 13:1 BL92

1 Caka ca makumi awiri ndi zitatu ca Yoasi mwana wa Ahaziya mfumu ya Yuda, Yoahazimwana wa Yehu analowa ufumu wace wa Israyeli ku Samariya, nakhala mfumu zaka khumi ndi zisanu ndi ziwiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 13

Onani 2 Mafumu 13:1 nkhani