2 Mafumu 13:20 BL92

20 Pamenepo Elisa anamwalira, ndipo anamuika. Ndipo magulu a Amoabu analowa m'dziko poyambira caka.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 13

Onani 2 Mafumu 13:20 nkhani