2 Mafumu 13:23 BL92

23 Koma Yehova analeza nao mtima, nawacitira cifundo, nawatembenukira; cifukwa ca cipangano cace ndi Abrahamu, Isake, ndi Yakobo, wosafuna kuwaononga, kapena kuwatayiratu pankhope pace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 13

Onani 2 Mafumu 13:23 nkhani