2 Mafumu 14:2 BL92

2 Ndiye wa zaka makumi awiri ndi zisanu polowa ufumu; nakhala mfumu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai m'Yerusalemu; dzina la mace ndiye Yoadana wa ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 14

Onani 2 Mafumu 14:2 nkhani