21 Ndipo anthu onse a Yuda anatenga Azariya, (ndiye Uziya), ndiye wa zaka khumi mphambu zisanu ndi cimodzi, namlonga ufumu m'malo mwa atate wace Amaziya,
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 14
Onani 2 Mafumu 14:21 nkhani