24 Nacita iye coipa pamaso pa Yehova, sanaleka zolakwa zonse za Yerobiamu mwana wa Nebati, zimene analakwitsa nazo Israyeli.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 14
Onani 2 Mafumu 14:24 nkhani