2 Mafumu 14:6 BL92

6 koma ana a ambandawo sanawapha, monga mwalembedwa m'buku la cilamulo ca Mose, m'mene adalamulira Yehova, ndi kuti, Atate asaphedwere ana, kapena ana kuphedwera atate; koma yense afere kulak wa kwa iye yekha.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 14

Onani 2 Mafumu 14:6 nkhani