27 Caka ca makumi asanu mphambu ziwiri ca Azariya mfumu ya Yuda, Peka mwana wa Remaliya analowa ufumu wace wa Israyeli m'Samariya, nakhala mfumu zaka makumi awiri.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:27 nkhani