30 Ndipo Hoseya mwana wa Ela anamcitira ciwembu Peka mwana wa Remaliya, namkantha, namupha, nakhala mfumu m'malo mwace caka ca makumi awiri ca Yotamu mwana wa Uziya.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:30 nkhani