2 Mafumu 15:33 BL92

33 Ndiye wa zaka makumi awiri mphambu: zisanu polowa ufumu wace, nakhalamfumu zaka khumi ndi zisanu ndi cimodzi m'Yerusalemu; ndipo dzina la mace ndiye Yerusa mwana wa Zadoki.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15

Onani 2 Mafumu 15:33 nkhani