35 Komatu sanaicotsa misanje; anthu anapherabe nsembe, nafukiza pamisanje. Iye anamanga cipata ca kumtunda ca nyumba ya Yehova.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:35 nkhani