18 Nacotsa ku nyumba ya Yehova malo ophimbika a pa Sabata adawamanga kunyumba, ndi polowera mfumu pofuma kunja, cifukwa ca mfumu ya Asuri.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 16
Onani 2 Mafumu 16:18 nkhani