2 Mafumu 16:6 BL92

6 Nthawi yomweyo Rezini mfumu ya Aramu anabwezera Elati kwa Aramu, napitikitsa Ayuda ku Elati; nadza Aaramu ku Elati, nakhala komweko kufikira lero lino.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 16

Onani 2 Mafumu 16:6 nkhani