2 Mafumu 17:15 BL92

15 Ndipo anakaniza malemba ace, ndi cipangano anacicita ndi makolo ao, ndi mboni zace anawacitira umboni nazo, natsata zopanda pace, nasanduka opanda pace, natsata amitundu owazinga, amene Yehova adawalamulira nao, kuti asacite monga iwowa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:15 nkhani