2 Mafumu 17:36 BL92

36 koma Yehova amene anakukwezani kukuturutsani m'dziko la Aigupto ndi mphamvu yaikuru, ndi dzanja lotambasuka, Iyeyu muzimuopa, ndi Iyeyu muzimgwadira, ndi Iyeyu muzimphera nsembe;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:36 nkhani