41 Ndipo amitundu awa anaopa Yehova, natumikira mafano ao osema; ana ao omwe, ndi zidzukulu zao zomwe, monga anacita makolo ao, momwemo iwo omwe mpaka lero lino.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17
Onani 2 Mafumu 17:41 nkhani