7 Kudatero, popeza ana a Israyeli adacimwira Yehova Mulungu wao, amene anawakweza kuwaturutsa m'dziko la Aigupto pansi pa dzanja la Farao mfumu ya Aigupto, ndipo anaopa milungu yina,
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17
Onani 2 Mafumu 17:7 nkhani