2 Mafumu 18:18 BL92

18 Ndipo m'mene adaitana mfumu, anawaturukira Eliyakimu mwana wa Hilikiya woyang'anira nyumba ya mfumu, ndi Sebina mlembi, ndi Yoa mwana wa Asafu wolemba mbiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:18 nkhani