2 Mafumu 18:2 BL92

2 Ndiye wa zaka makumi awiri ndi zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Abi mwana wa Zekariya.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:2 nkhani