2 Mafumu 18:22 BL92

22 Ndipo mukati kwa ine, Tikhulupirira Yehova Mulungu wathu; sindiye amene Hezekiya wamcotsera misanje yace ndi maguwa a nsembe ace, nati kwa Yuda ndi kwa Yerusalemu, Muzilambira pa guwa la nsembe pane m'Yerusalemu?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:22 nkhani