2 Mafumu 18:24 BL92

24 Posakhoza kutero, mudzabweza bwanji nkhope ya nduna imodzi ya anyamata ang'ono a mbuye wanga, ndi kukhulupirira Aigupto akupatse magareta ndi apakavalo?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:24 nkhani