2 Mafumu 18:27 BL92

27 Koma kazembeyo ananena nao, Ngati mbuyanga ananditumiza kwa mbuyako, ndi kwa iwe, kunena mau awa? si kwa anthu awa nanga okhala palinga, kuti akadye zonyansa zao, ndi kumwa mkodzo wao pamodzi ndi inu?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:27 nkhani