9 Ndipo kunali caka cacinai ca mfumu Hezekiya, ndico caka cacisanu ndi ciwiri ca Hoseya mwana wa Ela mfumu ya Israyeli Salimanezeri mfumu ya Asuri anakwerera Samariya, naumangira misasa.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18
Onani 2 Mafumu 18:9 nkhani